📚 New Reading Platform: Access your purchased books online Click here to start reading →
Your Shopping Cart
Total:
MK 0.00
DZIWANI ZAMATENDA OTHAMANGA MAGAZI

DZIWANI ZAMATENDA OTHAMANGA MAGAZI

By Henry Ndhlovu

Special Collections eBook Exclusives

MK10,000.00

Description:

Bukhuli lalembedwa pongochotsa ndime ina mubuku langa lotchedwa " *Turning Dreams Into Reality: Fighting Hypertension in Low-Resource Settings of Malawi through Moyowathu HealthCare Services".* 

Izi zachitika kutsatira pempho laena kuti ndiike padera ndime imeneyi ndipo ndikukhulupilira likhala laphindu kwaonse oliwelenga.

Ambiri tikudziwa mavuto omwe amadza chifukwa chamatenda othamanga magazi ndiye iyi ndimbali ina yothandizila kulimbana ndimatendawa.
 
Kuchokera  mundondomekoyi titha kulumikizana ndipo ngati nkotheka kuyezana BP ndikupatsana uphungu.

Filter Books

Subscribe to our newsletter